2 Samueli 4:10 BL92

10 muja munthu wina anandiuza kuti, Onani Sauli wamwalira, ndi kulingalira kuti alikubwera nao uthenga wabwino, ndinamgwira ndi kumupha ku Zikilaga, ndiyo mphotho yace ndinampatsa cifukwa ca uthenga wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4

Onani 2 Samueli 4:10 nkhani