2 Samueli 4:7 BL92

7 Koma polowa iwo m'nyumbamo iye ali cigonere pakama pace m'cipindamo, anamkantha, namupha namdula mutu wace, nautenga namuka njira ya kucidikha usiku wonse,

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4

Onani 2 Samueli 4:7 nkhani