2 Samueli 6:18 BL92

18 Pamene Davide adatsiriza kupereka nsembe yopsereza ndi zoyamika, iye anawadalitsa anthuwo m'dzina la Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:18 nkhani