10 Ndipo ndidzaikira anthu anga Israyeli malo, ndi kuwaoka kuti akakhale m'malo ao a iwo okha, osasunthikanso. Ndipo anthu a mphulupulu sadzawabvutanso, monga poyamba paja,
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7
Onani 2 Samueli 7:10 nkhani