13 Iye adzamangira dzina langa nyumba, ndipo ndidzakhazikitsa cimpando ca ufumu wace ku nthawi zonse.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7
Onani 2 Samueli 7:13 nkhani