2 Samueli 7:25 BL92

25 Ndipo tsopano, Yehova Mulungu, mau amene munalankhula za mnyamata wanu ndi za nyumba yace, muwalimbikitse ku nthawi zonse nimucite monga munalankhula.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7

Onani 2 Samueli 7:25 nkhani