27 Pakuti inu, Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, munaulula kwa mnyamata wanu kuti, Ndidzakumangira iwe nyumba; cifukwa cace mnyamata wanu analimbika mtima kupemphera pemphero gi kwa Inu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7
Onani 2 Samueli 7:27 nkhani