2 Samueli 7:7 BL92

7 M'malo monse ndinayendamo limodzi ndi ana onse a Israyeli kodi ndinanena ndi pfuko limodzi la Aisrayeli, limene ndinalamulira kudyetsa anthu anga Aisrayeli, kuti, Munalekeranji kundimangira nyumba yamikungudza?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7

Onani 2 Samueli 7:7 nkhani