2 Samueli 8:13 BL92

13 Ndipo Davide anamveketsa dzina lace pamene anabwera uko adakantha Aaramu m'cigwa ca mcere, ndiwo anthu zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8

Onani 2 Samueli 8:13 nkhani