2 Samueli 9:11 BL92

11 Pomwepo Ziba anati kwa mfumu, Monga mwa zonse mfumu mbuye wanga mulamulira mnyamata wanu, momwemo adzacita mnyamata wanu. Tsono Mefiboseti, anadya pa gome la Davide monga wina wa ana a mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9

Onani 2 Samueli 9:11 nkhani