2 Samueli 9:9 BL92

9 Pomwepo mfumu inaitana Ziba, mnyamata wa Sauli, ninena naye, Za Sauli zonse ndi za nyumba yace yonse ndampatsa mwana wa mbuye wako.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9

Onani 2 Samueli 9:9 nkhani