12 Usiku wapita, ndi dzuwa layandikira; cifukwa cace tibvule nchito za mdima, ntibvale camuna ca kuunika.
Werengani mutu wathunthu Aroma 13
Onani Aroma 13:12 nkhani