8 Musakhale ndi mangawa kwa munthu ali yense, koma kukondana ndiko; pakuti iye amene akondana ndi mnzace wakwanitsa lamulo.
Werengani mutu wathunthu Aroma 13
Onani Aroma 13:8 nkhani