Aroma 16:26 BL92

26 komai caonetsedwa tsopano, ndi kudziwidwa kwa anthu a mitundu yonse mwa malembo a aneneriwo, monga mwa lamulo la Mulungu wosatha, kuti amvere cikhulupiriro;

Werengani mutu wathunthu Aroma 16

Onani Aroma 16:26 nkhani