29 Kapena Mulungu ndiye wa Ayuda okha okha kodi? si wao wa amitundunso kodi? Bya, wa amitundunso:
Werengani mutu wathunthu Aroma 3
Onani Aroma 3:29 nkhani