11 Ndipo si cotero cokha, koma ife tikondwera ndi Mulungu mwa Ambuye wathu Yesu Kristu, amene talandira naye tsopano ciyanjanitso.
Werengani mutu wathunthu Aroma 5
Onani Aroma 5:11 nkhani