12 Cifukwa cace, monga ucimo unalowa m'dziko lapansi mwa munthu mmodzi, ndi imfa mwa ucimo; cotero imfa inafikira anthu onse, cifukwa kuti onse anacimwa.
Werengani mutu wathunthu Aroma 5
Onani Aroma 5:12 nkhani