6 Koma tsopano tinamasulidwa kucilamulo, popeza tinafa kwa ici cimene tinagwidwa naco kale; cotero kuti titumikire mu mzimu watsopano, si m'cilembo cakale ai.
Werengani mutu wathunthu Aroma 7
Onani Aroma 7:6 nkhani