Aroma 9:33 BL92

33 monganso kwalembedwa, kuti,8 Onani, ndikhazika m'Ziyoni mwala wakukhumudwa nao, ndi thanthwe lopunthwitsa;Ndipo 9 wakukhulupirira iye sadzacita manyazi.

Werengani mutu wathunthu Aroma 9

Onani Aroma 9:33 nkhani