Marko 12:4 BL92

4 Ndipo anatumanso kapolo wina kwa iwo; ndipo ameneyu anamlasa mutu, namcitira zomcititsa manyazi.

Werengani mutu wathunthu Marko 12

Onani Marko 12:4 nkhani