11 Ndipo Iye ananena nao, Kwa inu kwapatsidwa cinsinsi ca Ufumu wa Mulungu; koma kwa iwo ali kunja zonse zicitidwa m'mafanizo;
Werengani mutu wathunthu Marko 4
Onani Marko 4:11 nkhani