12 kuti kupenya apenye, koma asazindikire; ndipo kumva amve, koma asadziwitse; kuti pena angatembenuke, ndi kukhululukidwa.
Werengani mutu wathunthu Marko 4
Onani Marko 4:12 nkhani