29 Ndipo pomwepo kasupe wa nthenda yace adaphwa; ndipo anazindikira m'thupi kuti anaciritsidwa cibvutiko cace.
Werengani mutu wathunthu Marko 5
Onani Marko 5:29 nkhani