Marko 5:30 BL92

30 Ndipo pomwepo Yesu, pamene anazindikira mwa Iye yekha kuti mphamvu idaturuka mwa Iye, anapotoloka m'khamu, nanena, Ndani anakhudza zobvala zanga?

Werengani mutu wathunthu Marko 5

Onani Marko 5:30 nkhani