Marko 8:19 BL92

19 Pamene ndinawagawira anthu zikwi zisanu mikate isanu ija, munatola mitanga ingati yodzala ndi makombo? Ananena naye, Khumi ndi iwiri.

Werengani mutu wathunthu Marko 8

Onani Marko 8:19 nkhani