Marko 8:20 BL92

20 Ndipo mikate isanu ndi iwiri kwa anthu zikwi zinai, munatola malicero angati odzala ndi makombo? Ndipo ananena naye, Asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu Marko 8

Onani Marko 8:20 nkhani