20 Ndipo anadza naye kwa Iye; ndipo pakumuona, pomwepo mzimuwo unamng'amba koopsya; ndipo anagwa pansi nabvimbvinika ndi kucita thobvu.
Werengani mutu wathunthu Marko 9
Onani Marko 9:20 nkhani