Marko 9:21 BL92

21 Ndipo Iye anafunsa atate wace, kuti, Cimeneci cinayamba kumgwira liti? Ndipo anati, Cidamyamba akali mwana.

Werengani mutu wathunthu Marko 9

Onani Marko 9:21 nkhani