24 Ana akazi inu a Israyeli, mulirire Sauli,Amene anakubvekani ndi zofira zokometsetsa,Amene anaika zokometsetsa zagolidi pa zobvala zanu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1
Onani 2 Samueli 1:24 nkhani