23 Sauli ndi Jonatani anali okoma ndi okondweretsa m'miyoyo yao,Ndipo m'imfa yao sanasiyana; Anali nalo liwiro loposa ciombankanga,Anali amphamvu koposa mikango.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1
Onani 2 Samueli 1:23 nkhani