2 Samueli 1:22 BL92

22 Uta wa Jonatani sunabwerera,Ndipo lupanga la Sauli silinabwecera cabe,Pa mwazi wa ophedwa, pa mafuta a amphamvuwo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1

Onani 2 Samueli 1:22 nkhani