2 Samueli 1:6 BL92

6 Mnyamata wakumuuzayo nati, Pamene ndinangoyenda pa phiri la Giliboa, ndinaona, Sauli alikuyedzamira nthungo yace, ndi magareta ndi apakavalo anamyandikiza.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1

Onani 2 Samueli 1:6 nkhani