2 Samueli 10:18 BL92

18 Ndipo Aaramu anathawa pamaso pa Israyeli; Davide naphapo Aaramu apamagareta mazana asanu ndi awiri, ndi apakavalo zikwi makumi anai, nakantha Sobaki kazembe wa khamu lao, nafa iye pomwepo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:18 nkhani