19 Ndipo pamene mafumu onse, otumikira Hadarezeri, anaona kuti Aisrayeli anawapambana, iwo anapangana mtendere ndi Aisrayeli, nawatumikira, Comweco Aaramu anaopa kuwathandizanso ana a Amoni.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10
Onani 2 Samueli 10:19 nkhani