4 Comweco Hanuni anatenga anyamata a Davide nawameta ndebvu zao mbali imodzi, nadula zobvala zao pakati, kufikira m'matako ao, nawaleka amuke.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10
Onani 2 Samueli 10:4 nkhani