5 Pamene anaciuza Davide iye anatumiza anthu kukakomana nao; pakuti amunawo anacita manyazi akuru. Niti mfumu, Bakhalani ku Yeriko kufikira zamera ndebvuzanu; zitameramubwere.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10
Onani 2 Samueli 10:5 nkhani