2 Samueli 11:17 BL92

17 Ndipo akumudziwo anaturuka, namenyana ndi Yoabu; ndipo adagwapo anthu ena, ndiwo a anyamata a Davide; ndi Uriya Mhiti anafanso.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 11

Onani 2 Samueli 11:17 nkhani