2 Samueli 12:21 BL92

21 Pamenepo anyamata ace ananena naye, Ici mwacita nciani? Mwanayo akali moyo, munasala kudya ndi kumlira, koma pakufa mwanayo munyamuka ndi kudya,

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12

Onani 2 Samueli 12:21 nkhani