2 Samueli 12:22 BL92

22 Nati iye, Pamene mwanayo akali ndi moyo, ndinasala kudya ndi kulira, pakuti ndinati, Adziwa ndani kapena Yehova adzandicitira cifundo kuti mwanayo akhale ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12

Onani 2 Samueli 12:22 nkhani