23 Koma tsopano wafa, ndidzasaliranjinso kudya? Kodi ndikhoza kumbweza? Ine ndidzamuka kuli iye, koma iye sadzabweranso kwa ine.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12
Onani 2 Samueli 12:23 nkhani