24 Ndipo Davide anasangalatsa Bateseba mkazi wace, nalowa kwa iye, nagona naye; ndipo anabala mwana wamwamuna, namucha dzina lace Solomo. Ndipo Yehova anamkonda iye,
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12
Onani 2 Samueli 12:24 nkhani