2 Samueli 13:18 BL92

18 Ndipo iye anabvala cobvala ca mawanga mawanga, popeza ana akazi a mfumu okhala anamwali amabvala zotere. Ndipo mnyamata wace anamturutsa, napiringidza citseko atapita iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:18 nkhani