2 Samueli 13:19 BL92

19 Ndipo Tamara anathira phulusa pamutu pace, nang'amba cobvala ca mawanga mawanga cimene analikubvala, nagwira dzanja lace pamutu pace, namuka nayenda, nalira komveka.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:19 nkhani