23 Ndipo zitapita zaka ziwiri zathunthu, kunali kuti Abisalomu anali: nao osenga nkhosa zace ku Baalahazore pafupi pa Efraimu; ndipo Abisalomu anaitana ana amuna onse a mfumu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13
Onani 2 Samueli 13:23 nkhani