24 Abisalomu nafika kwa mfumu nati, Onani, ine mnyamata, wanu ndiri nao osenga nkhosa; inu mfumu ndi anyamata anu mupite nane mnyamata wanu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13
Onani 2 Samueli 13:24 nkhani