2 Samueli 13:25 BL92

25 Ndipo mfumu inati kwa Abisalomu, lai mwana wanga, tisapite tonse, kuti tingakucurukire. Ndipo iye anaiumirira koma inakana kupita; koma inamdalitsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:25 nkhani