2 Samueli 13:28 BL92

28 Ndipo Abisalomu anakamulira anyamata ace, nati, Inu mukhale maso, mtima wa Amnoni ukasekera ndi vinyo, ndipo ine ndikati kwa inu, Kanthani Amnoni; pamenepo mumuphe, musaope; sindine ndakulamulirani inu mulimbike, citani camuna.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:28 nkhani