2 Samueli 13:29 BL92

29 Ndipo anyamata a Abisalomu anamcitira Amnoni monga umo Abisalomu anawalamulira. Pomwepo ana amuna onse a mfumu ananyamuka, nakwera munthu yense pa nyuru yace, nathawa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:29 nkhani