2 Samueli 13:3 BL92

3 Koma Amnoni anali ndi bwenzi lace, dzina lace ndiye Jonadabu, mwana wa Sineya, mbale wa Davide. Ndipo Jonadabu anali munthu wocenjera ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:3 nkhani