2 Samueli 13:4 BL92

4 Nanena naye, Iwe mwana wa mfumu, uonderanji tsiku ndi tsiku? Sungandiuze kodi? Ndipo Amnoni anati kwa iye, Ndikonda Tamara, mlongo wa mbale wanga Abisalomu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:4 nkhani